Monga membala wa bungwe la Compassion padziko lonse lapansi, ndinu oyimira ana ndi achinyamata, ngakhale kuti simugwira ntchito ndi anawo. Pamaphunziro ofunikirawa, muphunzira momwe mungapewele mchitidwe wa nkhanza ndi kuchitapo kanthu pakachitika nkhanza, kulekeleledwa kapena kugwiritsidwa nthito mosayenera kwa ana ndi achinyamata. Maphunzirowa akuphatikizapo kuvomereza Malamulo akagwilidwe ka ntchito ka Compassion kokhuzana ndi chitetezo cha ana ndi achinyamata.