You must be a member of the ForChildren.com community to download resources. Click the buttons below to sign in or sign up!
| Category | Child Protection |
| Copyright Owner and Year | Compassion International - Malawi, 2023 |
Iyi ndi ndondomeko ya maphunziro a makolo ndi aliyense amene amasamalira mwana kuti aphunzire mmene angasamalire mwana, kumuteteza ku nkhanza ndi kumukonda mmene ambuye afunila.
Mwana kuti afikile maloto ndi kuthekera kwake akuyenera kukondedwa, kutetezedwa komanso Kusamalidwa. Makolo ndi omwe ali ndi udindo osamalila ndi kulera mwana wawo bwino, komatu osamalira ana ena sadziwa kuti mwana amusamale bwanji, amuteteze bwanji komanso amukonde bwanji.
Ichi ndi chifukwa chimene Compassion- Malawi yatanthauzila mlozowu mu chichewa kuti aliyense athe kuphunzila kaleledwe kabwino ka ana.
ForChildren.com is presented by Compassion International, a registered 501(c)3 non profit organization. All resources, courses, and discussions are intended for educational use only, not for profit.