You must be a member of the ForChildren.com community to download resources. Click the buttons below to sign in or sign up!
| Category | Child Protection |
| Copyright Owner and Year | Compassion International, 2024 |
Ana ambiri amachitilidwa nkhanza zosiyana siyana koma nzomvetsa chisoni kuti anawo sadziwa komanso sanena kuti akuchitilidwa nkhanza. Kanema uyu akulimbikitsa ana eni ake kuti aneneze anthu omwe akuwachita nkhanza kuti izi zinthe. Ana akuyenera kudziwa kuti iwo ndiwoyenera kukondedwa komanso kutetezedwa ku nkhanza za mtundu uliwonse.
ForChildren.com is presented by Compassion International, a registered 501(c)3 non profit organization. All resources, courses, and discussions are intended for educational use only, not for profit.